
single life pena moyo kufewa pena kumawawa azanga thupi likati litope nduzasuzumira windo pena angatuluke the left to the right but zero oh baby ngt nalakwisa ndipempha mkhululuke kaya mapemphero chonde abusa mundipempherere munthune nduziwa sinafune kumsiya ndati oh baby mkhululuke kaya mapemphero chonde abusa mundipempherere mwina zinthu zitha kusintha poti namalenga mitima malumikizisa pena ngat ungalire pena kuzatonthozedwa ngat nafedwa pena after reaching with friends oh baby chonde mkhululuke pazose nalakwisa ndipempha mkhululuke kaya abusa mundipempherere sinafune kumsiya zinachitika pena ndiye kuli ma friends aja kumazakuuza uja opanda khalidwe uja osasamba uja panti sagwirika amanyamula khosi day later iwe kuzangomva bae nzako uja amandifuna zulo shaaa oh baby ndipempha ukhululuke ngakhale maveravera anapanga tisiyane ndipempha ukhululuke abuse chonde mundipempherere sinafune kumsiya ddddj fobe mixing mixing the beat am out ukalakwisa kumapepesa
Type one line — get a full song with vocals in about a minute.
Clone your voice. Cover anything. Free to try.